.....

.....

Mady p freesty Hotest and badest (Daily freesty)

level yomwe amafuna atafika ine NDINADUTSA/ amangokhala chabe ndimakani OPUSA/ olo zoti 1 + 1 ndi 2 atha ku TSUTSA/ nde sangavomeleze kuti ndine LUSA/ malyric okhaokha a CHICHEWA/ koma ndimadabwa kundifananitsa ndi anthu ONSEWA/ kuposa HIV muyenera kundi PEWA/ kulowa Hardcore koma mental kuma FEWA/ Mady AKA dada,Messiah,olo MJIBA/ ndimagwetsa ma track(truck) ana akugwetsa ma WHEELBAR